Masalmo 96:13 BL92

13 Pamaso pa Yehova, pakuti akudza;Pakuti akudza kudzaweruza dziko lapansi:Adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi cilungamo,Ndi mitundu ya anthu ndi coonadi.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 96

Onani Masalmo 96:13 nkhani